Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Eksodo 38:10 - Buku Lopatulika

10 nsichi zake makumi awiri, ndi makamwa ao makumi awiri, amkuwa; zokowera za nsichi ndi mitanda yake zasiliva.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 nsichi zake makumi awiri, ndi makamwa ao makumi awiri, amkuwa; zokowera za nsichi ndi mitanda yake zasiliva.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Nsanamira zake makumi aŵiri, pamodzi ndi masinde ake makumi aŵiri, zonsezo zinali zamkuŵa, koma ngoŵe za pa nsanamirazo, pamodzi ndi mitanda yake, zinali zasiliva.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Anapanganso mizati makumi awiri, matsinde makumi awiri amkuwa ndi ngowe zasiliva ndi zingwe za mizatiyo.

Onani mutuwo Koperani




Eksodo 38:10
3 Mawu Ofanana  

ndi nsichi zake makumi awiri, ndi makamwa ao makumi awiri akhale amkuwa; zokowera za nsichi ndi mitanda yake zikhale zasiliva.


Ndi pa mbali ya kumpoto mikono zana limodzi, nsichi zake makumi awiri, ndi makamwa ake makumi awiri, amkuwa; zokowera za nsichi ndi mitanda yake yasiliva.


Ndipo anapanga bwalo; pa mbali ya kumwera, kumwera, nsalu zotchingira za pabwalo zinali za bafuta wa thonje losansitsa, mikono zana limodzi;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa