Eksodo 36:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Mose analamulira, ndipo anamveketsa mau mu chigono chonse, ndi kuti, Asaonjezere ntchito ya ku chopereka cha malo opatulika, ngakhale mwamuna ngakhale mkazi. Tero anawaletsa anthu asabwere nazo zina. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Mose analamulira, ndipo anamveketsa mau mwa chigono chonse, ndi kuti, Asaonjezere ntchito ya ku chopereka cha malo opatulika, ngakhale mwamuna ngakhale mkazi. Tero anawaletsa anthu asabwere nazo zina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Motero Mose adalamula anthu m'mahema monse kuti, “Mwamuna aliyense ndi mkazi aliyense asaperekenso zopereka zomangira malo opatulika.” Motero anthu adaleka kubwera ndi zopereka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Choncho Mose analamulira ndipo analengeza mu msasa onse, “Mwamuna kapena mayi aliyense asaperekenso chopereka chilichonse cha ku malo wopatulika.” Choncho anthu analetsedwa kubweretsa zambiri, Onani mutuwo |