Eksodo 33:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo ana a Israele anazichotsera zokometsera zao kuyambira paphiri la Horebu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo ana a Israele anazichotsera zokometsera zao kuyambira pa phiri la Horebu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Motero kuyambira ku phiri lija la Horebu, Aisraele sadavalenso zokongoletsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kotero Aisraeli anavula zodzikometsera zawo pa phiri la Horebu. Onani mutuwo |