Eksodo 33:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo pamene anthu anamva mau awa oipa anachita chisoni; ndipo panalibe mmodzi anavala zokometsera zake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo pamene anthu anamva mau awa oipa anachita chisoni; ndipo panalibe mmodzi anavala zokometsera zake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono anthu atamva mau oopsaŵa, adayamba kulira, ndipo panalibe ndi mmodzi yemwe amene adavala zovala zokongola. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Anthu atamva mawu owopsawa, anayamba kulira ndipo palibe anavala zodzikometsera. Onani mutuwo |