Eksodo 33:23 - Buku Lopatulika23 ndipo pamene ndichotsa dzanja langa udzaona m'mbuyo mwanga; koma nkhope yanga siidzaoneka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 ndipo pamene ndichotsa dzanja langa udzaona m'mbuyo mwanga; koma nkhope yanga siidzaoneka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Kenaka ndichotsa dzanja langa, ndipo undiwona kumsana, koma nkhope yanga suiwona ai.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Kenaka ine ndidzachotsa dzanja langa ndipo iwe udzaona msana wanga, koma nkhope yanga sidzaoneka.” Onani mutuwo |