Eksodo 33:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo anati, Ndionetsenitu ulemerero wanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo anati, Ndionetsenitu ulemerero wanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Apo Mose adapempha Chauta kuti, “Chonde mundiwonetse ulemerero wanu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Kenaka Mose anati, “Tsopano ndionetseni ulemerero wanu.” Onani mutuwo |