Eksodo 26:8 - Buku Lopatulika8 Utali wake wa nsalu imodzi ndiwo mikono makumi atatu, ndi kupingasa kwake kwa nsalu imodzi ndiko mikono inai; nsalu khumi ndi imodzi zikhale za muyeso womwewo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Utali wake wa nsalu imodzi ndiwo mikono makumi atatu, ndi kupingasa kwake kwa nsalu imodzi ndiko mikono inai; nsalu khumi ndi imodzi zikhale za muyeso womwewo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Muutali mwake nsalu iliyonse ikhale mamita 14, ndipo muufupi mwake pafupi mamita aŵiri. Zonsezo zikhale zofanana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Nsalu zonse khumi ndi imodzi zikhale zofanana. Mulitali mwake mukhale mamita khumi ndi anayi ndipo mulifupi mwake mukhale mamita awiri. Onani mutuwo |