Eksodo 24:2 - Buku Lopatulika2 ndipo Mose yekha ayandikire kwa Yehova; koma asayandikire iwowa; ndi anthunso asakwere naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 ndipo Mose yekha ayandikire kwa Yehova; koma asayandikire iwowa; ndi anthunso asakwere naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mose yekha ndiye andiyandikire, koma enawo asafike pafupi. Anthu ena onse nawonso asabwere ndi Moseyo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Koma Mose yekha ayandikire Yehova, ndipo enawo asayandikire. Komanso anthu ena onse asakwere nawe ku phiri kuno.” Onani mutuwo |