Eksodo 23:30 - Buku Lopatulika30 Ndidzawaingitsa pang'onopang'ono pamaso pako, kufikira utachuluka, ndi kulandira dziko cholowa chako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Ndidzawaingitsa pang'onopang'ono pamaso pako, kufikira utachuluka, ndi kulandira dziko cholowa chako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Koma ndidzaŵapirikitsa pang'onopang'ono, mpaka mutabala ana ambiri amene angathe kutenga dzikolo, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndidzawathamangitsa pangʼonopangʼono mpaka inu mutachuluka kokwanira mwakuti nʼkutenga dzikolo. Onani mutuwo |