Eksodo 23:21 - Buku Lopatulika21 Musamalire iye, ndi kumvera mau ake; musamuwawitsa mtima, pakuti sadzakhululukira zolakwa zanu; popeza dzina langa lili m'mtima mwake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Musamalire iye, ndi kumvera mau ake; musamwawitsa mtima, pakuti sadzakhululukira zolakwa zanu; popeza dzina langa lili m'mtima mwake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Mumvere iyeyo, ndipo mumvetse zimene akunena. Musamchite zaupandu, chifukwa sadzakhululukira tchimo lotere. Iye akuchita zimenezi m'dzina langa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Muzimumvera ndi kumvetsetsa zimene akunena. Musamuwukire chifukwa sadzakhululuka kuwukira kwanu, pakuti akuchita zimenezi mʼdzina langa. Onani mutuwo |