Eksodo 23:17 - Buku Lopatulika17 Katatu m'chaka amuna onse azioneka pamaso pa Ambuye Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Katatu m'chaka amuna onse azioneka pamaso pa Ambuye Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Anthu aamuna onse aziwonekera pamaso pa Ine Chauta pa masiku atatu ameneŵa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 “Amuna onse azionekera pamaso pa Ambuye Yehova katatu pa chaka. Onani mutuwo |