Eksodo 22:26 - Buku Lopatulika26 Ukati ulandire chikole kaya chovala cha mnansi wako, koma polowa dzuwa uchibwezere kwa iye; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ukati ulandire chikole kaya chovala cha mnansi wako, koma polowa dzuwa uchibwezere kwa iye; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Mukatenga mwinjiro wa munthu wina ngati chigwiriro kuti adzakulipireni, muubweze dzuŵa lisanaloŵe, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Mukatenga chovala cha mnzanu kuti chikhale chikole mumubwezere dzuwa lisanalowe Onani mutuwo |