Eksodo 20:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo anthu anaima patali, koma Mose anayandikiza ku mdima waukulu kuli Mulungu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo anthu anaima patali, koma Mose anayandikiza ku mdima waukulu kuli Mulungu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Koma anthu ankaima kutali, Mose yekha ndiye adayandikira mtambo wamdima m'mene munali Mulungu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Anthu aja anayima patali koma Mose anayandikira mtambo wakuda kumene kunali Mulungu. Onani mutuwo |