Eksodo 18:11 - Buku Lopatulika11 Tsopano ndidziwa kuti Yehova ali wamkulu ndi milungu yonse, pakuti momwe anadzikuza okha momwemo anawaposa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Tsopano ndidziwa kuti Yehova ali wamkulu ndi milungu yonse, pakuti momwe anadzikuza okha momwemo anawaposa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Tsopano ndikudziŵa kuti Chauta ndi wamkulu kupambana milungu ina yonse, chifukwa adapulumutsa Aisraele kwa Aejipito, pamene Aejipitowo ankaŵanyoza.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tsopano ndikudziwa kuti Yehova ndi wopambana milungu ina yonse, pakuti anachita izi kwa amene ananyoza Israeli.” Onani mutuwo |