Eksodo 16:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo kunakhala, pakunena Aroni ndi khamu lonse la ana a Israele kuti iwo anatembenukira kuchipululu, ndipo, taonani, ulemerero wa Yehova unaoneka mumtambo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo kunakhala, pakunena Aroni ndi khamu lonse la ana a Israele kuti iwo anatembenukira kuchipululu, ndipo, taonani, ulemerero wa Yehova unaoneka mumtambo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono Aroni akulankhula ndi khamu lonse lija, khamulo lidatembenuka kupenya ku chipululu, ndipo ulemerero wa Chauta udaoneka mu mtambo mwadzidzidzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pamene Aaroni amayankhula ndi gulu lonse la Aisraeli, iwo anayangʼana ku chipululu, ndipo ulemerero wa Yehova umaoneka mu mtambo. Onani mutuwo |