Eksodo 13:6 - Buku Lopatulika6 Masiku asanu ndi awiri uzikadya mkate wopanda chotupitsa, ndipo tsiku lachisanu ndi chiwiri likhale la madyerero a Yehova; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Masiku asanu ndi awiri uzikadya mkate wopanda chotupitsa, ndipo tsiku lachisanu ndi chiwiri likhale la madyerero a Yehova; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Pa masiku asanu ndi aŵiri, muzidzadya buledi wosafufumitsa, ndipo pa tsiku lachisanu ndi chiŵirilo pazidzakhala chikondwerero cha Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Muzidzadya buledi wopanda yisiti kwa masiku asanu ndi awiri ndipo tsiku lachisanu ndi chiwirilo muzichita chikondwerero cha Yehova. Onani mutuwo |