Eksodo 12:49 - Buku Lopatulika49 Pakhale lamulo lomweli pa wobadwa m'dziko, ndi pa mlendo wakukhala pakati pa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201449 Pakhale lamulo lomweli pa wobadwa m'dziko, ndi pa mlendo wakukhala pakati pa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa49 Lamulo limeneli ndi la mbadwa yeniyeni ya Israele, ndiponso la mlendo woumbalidwa amene ali pakati panu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero49 Lamulo limeneli likhudza mbadwa ngakhalenso alendo wochita mdulidwe wokhala pakati panu. Onani mutuwo |