Eksodo 11:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo kudzakhala kulira kwakukulu m'dziko lonse la Ejipito, kunalibe kunzake kotere, sikudzakhalanso kunzake kotere. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo kudzakhala kulira kwakukulu m'dziko lonse la Ejipito, kunalibe kunzake kotere, sikudzakhalanso kunzake kotere. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 M'dziko lonse la Ejipito mudzakhala maliro okhaokha amene sadaonekepo nkale lonse, ndipo sadzaonekanso. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Kudzakhala kulira kwakukulu mʼdziko lonse la Igupto, kumene sikunachitikepo ndipo sikudzachitikanso. Onani mutuwo |