Eksodo 11:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Mose anati, Atero Yehova, Monga pakati pa usiku ndidzatuluka Ine kunka pakati pa Aejipito; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Mose anati, Atero Yehova, Monga pakati pa usiku ndidzatuluka Ine kunka pakati pa Aejipito; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Tsono Mose adauza Farao kuti, “Chauta akunena kuti, ‘Ndiyenda pakati pa Aejipito pakati pa usiku, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Tsono Mose anawuza Farao kuti, “Pakati pa usiku, Yehova adzayenda pakati pa anthu a ku Igupto. Onani mutuwo |