Eksodo 10:4 - Buku Lopatulika4 pakuti ukakana kulola anthu anga amuke, taona, mawa ndidzafikitsa dzombe m'dziko lako; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 pakuti ukakana kulola anthu anga amuke, taona, mawa ndidzafikitsa dzombe m'dziko lako; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ukakanabe kuŵalola kuti apite, ndikugwetsera dzombe maŵa m'dziko mwako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ngati ukana kuwalola, ndigwetsa dzombe mʼdziko lako lino mawa. Onani mutuwo |