Eksodo 10:20 - Buku Lopatulika20 Koma Yehova analimbitsa mtima wa Farao, ndipo sanalole ana a Israele amuke. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Koma Yehova analimbitsa mtima wa Farao, ndipo sanalole ana a Israele amuke. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Koma Chauta adamuumitsabe mtima Farao, ndipo sadaŵalole Aisraele kuti apite. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Koma Yehova anawumitsa mtima wa Farao, ndipo sanalole kuti Aisraeli apite. Onani mutuwo |