Danieli 8:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo ndinamva mau a munthu pakati pa magombe a Ulai, naitana, nati, Gabriele, zindikiritsa munthuyu masomphenyawo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo ndinamva mau a munthu pakati pa magombe a Ulai, naitana, nati, Gabriele, zindikiritsa munthuyu masomphenyawo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndipo ndinamva mawu a munthu kuchokera mʼmbali mwa mtsinje wa Ulai akuyitana kuti, “Gabrieli, muwuze munthuyu tanthauzo la masomphenyawo.” Onani mutuwo |