Danieli 7:26 - Buku Lopatulika26 Koma woweruza mlandu adzakhalako, ndipo adzachotsa ulamuliro wake, kuutha ndi kuuononga kufikira chimaliziro. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Koma woweruza mlandu adzakhalako, ndipo adzachotsa ulamuliro wake, kuutha ndi kuuononga kufikira chimaliziro. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 “ ‘Koma bwalo lidzapereka chiweruzo, ndipo mphamvu zake zidzalandidwa ndi kuwonongedwa kotheratu mpaka muyaya. Onani mutuwo |