Danieli 6:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo akulu awa ndi akalonga anasonkhana kwa mfumu mofulumira, natero nayo, Mfumu Dariusi, mukhale ndi moyo chikhalire. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo akulu awa ndi akalonga anasonkhana kwa mfumu mofulumira, natero nayo, Mfumu Dariusi, mukhale ndi moyo chikhalire. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Choncho akalonga ndi nduna pamodzi anapita kwa mfumu ndipo anati: “Inu mfumu Dariyo, mukhale ndi moyo wautali! Onani mutuwo |