Danieli 5:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo inu mwana wake, Belisazara inu, simunadzichepetse m'mtima mwanu, chinkana munazidziwa izi zonse; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo inu mwana wake, Belisazara inu, simunadzichepetsa m'mtima mwanu, chinkana munazidziwa izi zonse; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 “Koma inu mwana wake, Belisazara, simunadzichepetse, ngakhale kuti mumadziwa zonsezi. Onani mutuwo |