Danieli 4:20 - Buku Lopatulika20 Mtengo mudauona umene unakula, nukhala wolimba, nufikira kumwamba msinkhu wake, nuonekera padziko lonse lapansi, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Mtengo mudauona umene unakula, nukhala wolimba, nufikira kumwamba msinkhu wake, nuonekera pa dziko lonse lapansi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Mtengo munawuona uja, umene unkakulirakulira kwambiri ndi kulimba, ndi msonga yake inafika mlengalenga, ndi kuonekera ku dziko lonse lapansi, Onani mutuwo |