Danieli 3:13 - Buku Lopatulika13 Pamenepo Nebukadinezara, mumkwiyo ndi mu ukali wake, anawauza abwere nao Sadrake, Mesaki, ndi Abedenego. Ndipo anabwera nao amunawa kwa mfumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Pamenepo Nebukadinezara, mumkwiyo ndi m'ukali wake, anawauza abwere nao Sadrake, Mesaki, ndi Abedenego. Ndipo anabwera nao amunawa kwa mfumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Tsono Nebukadinezara anakwiya ndi kupsa mtima kwambiri, ndipo anayitanitsa Sadirake, Mesaki ndi Abedenego. Choncho amuna awa anabwera pamaso pa mfumu, Onani mutuwo |