Danieli 11:34 - Buku Lopatulika34 Ndipo pakugwa iwo adzathandizidwa ndi thandizo laling'ono; koma ambiri adzaphatikizana nao ndi mau osyasyalika. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Ndipo pakugwa iwo adzathandizidwa ndi thandizo laling'ono; koma ambiri adzaphatikizana nao ndi mau osyasyalika. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Pa nthawi yozunzikayi ena adzawathandiza pangʼono, koma ambiri othandizawo adzakhala achinyengo. Onani mutuwo |