Danieli 11:26 - Buku Lopatulika26 Inde iwo akudyako chakudya chake adzamuononga; ndi ankhondo ake adzasefukira, nadzagwa ambiri ophedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Inde iwo akudyako chakudya chake adzamuononga; ndi ankhondo ake adzasefukira, nadzagwa ambiri ophedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Amene amadya chakudya ndi mfumu adzamuukira; gulu lake lankhondo lidzagonjetsedwa, ndipo ambiri adzafera ku nkhondo. Onani mutuwo |