Danieli 1:6 - Buku Lopatulika6 Mwa awa tsono munali a ana a Yuda, Daniele, Hananiya, Misaele, ndi Azariya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Mwa awa tsono munali a ana a Yuda, Daniele, Hananiya, Misaele, ndi Azariya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Pakati pa amenewa panali ena ochokera ku Yuda: Danieli, Hananiya, Misaeli ndi Azariya. Onani mutuwo |