Danieli 1:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo mfumu inauza Asipenazi mkulu wa adindo kuti abwere nao ena a ana a Israele, a mbeu ya mafumu, ndi ya akalonga; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo mfumu inauza Asipenazi mkulu wa adindo kuti abwere nao ena a ana a Israele, a mbeu ya mafumu, ndi ya akalonga; Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Tsono mfumu inalamula Asipenazi, mkulu wa nduna zake kuti abwere nawo ena mwa Aisraeli ochokera mʼbanja laufumu ndi la olemekezeka, Onani mutuwo |