Akolose 2:9 - Buku Lopatulika9 pakuti mwa Iye chikhalira chidzalo cha Umulungu m'thupi, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 pakuti mwa Iye chikhalira chidzalo cha Umulungu m'thupi, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pakuti m'thupi la Khristu umulungu wonse umakhalamo wathunthu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pakuti mʼthupi la Khristu mumakhala umulungu wonse wathunthu. Onani mutuwo |