Akolose 2:4 - Buku Lopatulika4 Ichi ndinena, kuti munthu asakusokeretseni inu ndi mau okopakopa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ichi ndinena, kuti munthu asakusokeretseni inu ndi mau okopakopa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ndikunenatu zimenezi, kuwopa kuti wina aliyense angakukopeni ndi mau onyenga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndikukuwuzani zimenezi kuti wina aliyense asakunamizeni ndi kukukopani ndi mawu ake. Onani mutuwo |