Akolose 1:8 - Buku Lopatulika8 amenenso anatifotokozera chikondi chanu mwa Mzimu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 amenenso anatifotokozera chikondi chanu mwa Mzimu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndiye amene adatidziŵitsa za chikondi chomwe Mzimu Woyera adaika mwa inu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Iye anatiwuza za chikondi chanu chimene Mzimu anakupatsani. Onani mutuwo |