Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Ahebri 7:20 - Buku Lopatulika

20 Ndipo monga momwe sikudachitike kopanda lumbiro; (pakuti iwotu anayesedwa ansembe kopanda lumbiro;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 Ndipo monga momwe sikudachitika kopanda lumbiro; (pakuti iwotu anayesedwa ansembe kopanda lumbiro;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 Chinanso nchakuti Mulungu adaachita kulumbira. Amene ankaloŵa unsembe kale lija ankatenga udindo waowo popanda lumbiro.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 Izi sizinachitiketu wopanda lumbiro. Ena ankakhala ansembe popanda lumbiro.

Onani mutuwo Koperani




Ahebri 7:20
5 Mawu Ofanana  

Yehova walumbira, ndipo sadzasintha, Inu ndinu wansembe kosatha monga mwa chilongosoko cha Melkizedeki.


Ndipo iwe ndi ana ako aamuna pamodzi ndi iwe muchite ntchito yanu ya nsembe, pa zonse za ku guwa la nsembe, ndi za m'kati mwa nsalu yotchinga; ndipo mutumikire; ndikupatsani ntchito yanu ya nsembe, utumiki wopatsika kwaulere; koma mlendo wakuyandikiza amuphe.


Monga anenanso mwina, Iwe ndiwe wansembe wa nthawi zonse monga mwa dongosolo la Melkizedeki.


(pakuti chilamulo sichinachitire kanthu kakhale kopanda chilema), ndipo kulinso kulowa nacho chiyembekezo choposa, chimene tiyandikira nacho kwa Mulungu.


koma Iye ndi lumbiro mwa Iye amene anenana kwa Iye, Walumbira Ambuye ndipo sadzalapa, iwe ndiwe wansembe nthawi yosatha).


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa