Ahebri 2:8 - Buku Lopatulika8 mudagonjetsa zonse pansi pa mapazi ake. Pakuti muja adagonjetsa zonse kwa iye, sanasiyepo kanthu kosamgonjera iye. Koma sitinayambe tsopano apa kuona zonse zimgonjera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 mudagonjetsa zonse pansi pa mapazi ake. Pakuti muja adagonjetsa zonse kwa iye, sanasiyapo kanthu kosamgonjera iye. Koma sitinayamba tsopano apa kuona zonse zimgonjera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 ndipo mudampatsa ulamuliro pa zinthu zonse.” Tsono ngati Mulungu adapatsa munthu ulamuliro pa zinthu zonse, palibe kanthu kamene sikali mu ulamuliro wake. Komabe m'mene zinthu ziliri tsopano sitikuwona kuti zonse zakhaladi mu ulamuliro wakewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Munamupatsa ulamuliro pa zinthu zonse.” Poyika zinthu zonse pansi pa ulamuliro wake, Mulungu sanasiye kanthu kamene sikali mu ulamuliro wake. Koma nthawi ino sitikuona zinthu pansi pa ulamuliro wake. Onani mutuwo |