Afilipi 2:18 - Buku Lopatulika18 momwemonso kondwerani inu, nimukondwere pamodzi ndi ine. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 momwemonso kondwerani inu, nimukondwere pamodzi ndi ine. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Chimodzimodzi inunso muzikondwa, ndi kusangalala nane pamodzi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Chomwechonso, inu khalani okondwa ndi osangalala nane pamodzi. Onani mutuwo |