Afilipi 1:26 - Buku Lopatulika26 kuti kudzitamandira kwanu kuchuluke mu Khristu Yesu mwa ine, mwa kukhalanso ine kwa inu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 kuti kudzitamandira kwanu kuchuluke m'Khristu Yesu mwa ine, mwa kukhalanso ine kwa inu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Motero pamene ndidzafikanso kwanuko, mudzakhala ndi zifukwa zochuluka zonyadira Khristu Yesu chifukwa cha ine. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 kuti pokhala nanunso, kudzitamandira kwanu mwa Khristu Yesu kudzasefukire chifukwa cha ine. Onani mutuwo |