Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Afilipi 1:24 - Buku Lopatulika

24 koma kukhalabe m'thupi ndiko kufunika koposa, chifukwa cha inu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 koma kukhalabe m'thupi ndiko kufunika koposa, chifukwa cha inu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Koma kwinakunso nkofunika kwambiri kuti ndikhale moyo chifukwa cha inuyo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Komanso nʼkofunika kwambiri kuti ndikhalebe mʼthupi chifukwa cha inu.

Onani mutuwo Koperani




Afilipi 1:24
5 Mawu Ofanana  

Koma ndinena Ine choonadi ndi inu; kuyenera kwa inu kuti ndichoke Ine; pakuti ngati sindichoka, Nkhosweyo sadzadza kwa inu; koma ngati ndipita ndidzamtuma Iye kwa inu.


Koma ngati kukhala ndi moyo m'thupi ndiko chipatso cha ntchito yanga, sindizindikiranso chimene ndidzasankha.


Koma ndipanidwa nazo ziwirizi, pokhala nacho cholakalaka cha kuchoka kukhala ndi Khristu, ndiko kwabwino koposaposatu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa