Aefeso 4:12 - Buku Lopatulika12 kuti akonzere oyera mtima kuntchito ya utumiki, kumangirira thupi la Khristu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 kuti akonzere oyera mtima kuntchito ya utumiki, kumangirira thupi la Khristu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ntchito yao inali yakuti akonzeretu anthu a Mulungu kuti akagwire ntchito yotumikira, ndi kulimbitsa Mpingo umene uli thupi la Khristu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ntchito yawo ndi kukonza oyera mtima kuti agwire ntchito ya utumiki kuti thupi la Khristu lilimbikitsidwe. Onani mutuwo |