Aefeso 3:7 - Buku Lopatulika7 umene anandikhalitsa mtumiki wake monga mwa mphatso ya chisomo cha Mulungu, chimene anandipatsa ine, monga mwa machitidwe a mphamvu yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 umene anandikhalitsa mtumiki wake monga mwa mphatso ya chisomo cha Mulungu, chimene anandipatsa ine, monga mwa machitidwe a mphamvu yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mwa kukoma mtima kwake Mulungu adandisandutsa wolalika Uthenga Wabwino umenewu, ndipo pakutero adaonetsapo mphamvu yake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mwachisomo cha Mulungu ndi mphamvu zake, ine ndinasanduka mtumiki wa Uthenga Wabwinowu. Onani mutuwo |