Aefeso 1:22 - Buku Lopatulika22 ndipo anakonza zonse pansi pa mapazi ake, nampatsa Iye akhale mutu pamutu pa zonse, kwa Mpingo Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 ndipo anakonza zonse pansi pa mapazi ake, nampatsa Iye akhale mutu pamtu pa zonse, kwa Mpingo Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Mulungu adagonjetsa zonse kuti zikhale pansi pa mapazi a Khristu, ndipo adamkhazika pamwamba pa zonse kuti akhale mutu wa Mpingo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Ndipo Mulungu anayika zinthu zonse pansi pa mapazi ake ndi kumusankha Iyeyo kukhala mutu pa chilichonse chifukwa cha mpingo, Onani mutuwo |