2 Timoteyo 3:9 - Buku Lopatulika9 Koma sadzapitirirapo; pakuti kupusa kwao kudzaonekeratu kwa onse, monganso kupusa kwa iwo aja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Koma sadzapitirirapo; pakuti kupusa kwao kudzaonekeratu kwa onse, monganso kupusa kwa iwo aja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Koma sadzapitirira nazo, pakuti anthu onse adzaona kupusa kwao, monga momwe zidaachitikiranso ndi Yane uja ndi Yambere. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Koma sadzapita nazo patali kwambiri zimenezi, pakuti anthu onse adzaona kupusa kwawo monga anachitira Yanesi ndi Yambere. Onani mutuwo |