Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 3:33 - Buku Lopatulika

33 Ndipo mfumu inanenera Abinere nyimbo iyi ya maliro, niti, Kodi Abinere anayenera kufa ngati chitsiru?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

33 Ndipo mfumu inanenera Abinere nyimbo iyi ya maliro, niti, Kodi Abinere anayenera kufa ngati chitsiru?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

33 Polira maliro a Abinere mfumu Davide ankati, “Abinere nkufa motere, monga m'mene chimafera chitsiru?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

33 Mfumu inayimba nyimbo iyi ya maliro a Abineri: “Abineri nʼkufa motere monga mmene chimafera chitsiru.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 3:33
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Davide analirira Saulo ndi Yonatani mwana wake ndi nyimbo iyi ya maliro;


Manja anu sanamangidwe, mapazi anu sanalongedwe m'zigologolo; monga munthu wakugwa ndi anthu oipa momwemo mudagwa inu. Ndipo anthu onse anamliranso.


Ndipo Yeremiya anamlembera Yosiya nyimbo yomlira; ndi oimbira onse, amuna ndi akazi, amanena za Yosiya nyimbo za maliro zao mpaka lero lino; naziika zikhale lemba mu Israele; taonani, zilembedwa mu Nyimbo za Maliro.


M'kamwa mwa wopusa mumuononga, milomo yake ikhala msampha wa moyo wake.


Monga nkhwali iumatira pa mazira amene sinaikire, momwemo iye amene asonkhanitsa chuma, koma mosalungama; pakati pa masiku ake chidzamsiya iye, ndipo pa chitsirizo adzakhala wopusa.


Iyi ndi nyimbo ya maliro adzalira nayo, ana aakazi a amitundu adzachita nayo maliro; adzalirira nayo Ejipito ndi aunyinji ake onse, ati Ambuye Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa