2 Samueli 3:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo Abinere analankhula nao akulu a Israele nanena nao, Inu munayamba kale kufuna Davide akhale mfumu yanu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo Abinere analankhula nao akulu a Israele nanena nao, Inu munayamba kale kufuna Davide akhale mfumu yanu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Pambuyo pake Abinere pokambirana ndi atsogoleri a Aisraele, adaŵauza kuti, “Nthaŵi yapitayi mwakhala mukufuna Davide kuti akhale mfumu yanu yokulamulani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Abineri anakambirana ndi akuluakulu a Israeli ndipo anati, “Kwa kanthawi mwakhala mukufuna kulonga Davide kuti akhale mfumu yanu. Onani mutuwo |