2 Samueli 3:15 - Buku Lopatulika15 Pomwepo Isiboseti anatumiza namchotsera kwa mwamuna wake, kwa Palatiele mwana wa Laisi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Pomwepo Isiboseti anatumiza namchotsera kwa mwamuna wake, kwa Palatiele mwana wa Laisi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Pamenepo Isiboseti adatuma anthu kuti akamtenge Mikalayo kwa mwamuna wake Palatiele, mwana wa Laisi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Kotero Isi-Boseti analamulira ndipo anakamutenga kwa mwamuna wake Palitieli mwana wa Laisi. Onani mutuwo |