2 Samueli 21:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo kunali chitapita ichi, kunalinso nkhondo ndi Afilisti ku Gobu; pamenepo Sibekai Muhusa anapha Safi, ndiye wa ana a Rafa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo kunali chitapita ichi, kunalinso nkhondo ndi Afilisti ku Gobu; pamenepo Sibekai Muhusa anapha Safi, ndiye wa ana a Rafa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Pambuyo pake nkhondo idabukanso ndi Afilisti ku Gobu. Pamenepo Sibekai Muhusa, adapha Safu, amene analinso mmodzi mwa zidzukulu za Arefaimu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Patapita nthawi, panali nkhondo ina ndi Afilisti ku Gobu. Pa nthawi imeneyo Sibekai Mhusati anapha Safu, mmodzi mwa zidzukulu za Arefai. Onani mutuwo |