2 Samueli 20:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo anapyola mafuko onse a Israele kufikira ku Abele ndi ku Betimaaka, ndi kwa Abikiri onse; iwo nasonkhana pamodzi namlondolanso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo anapyola mafuko onse a Israele kufikira ku Abele ndi ku Betimaaka, ndi kwa Abikiri onse; iwo nasonkhana pamodzi namlondolanso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Sheba adapita ndithu kubzola mafuko onse a Aisraele mpaka kukafika ku Abele wa ku Betemaki. Abikiri onse adasonkhana, naloŵa naye mumzindamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Seba anadutsa mafuko onse a Israeli mpaka ku Abeli ndi Beti-Maaka ndiponso chigawo chonse cha Abeli, amene anasonkhana pamodzi ndi kumutsata iye. Onani mutuwo |