2 Samueli 2:31 - Buku Lopatulika31 Koma anyamata a Davide anakantha anthu a Benjamini ndi a Abinere, namwalira mazana atatu mphambu makumi asanu ndi limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Koma anyamata a Davide anakantha anthu a Benjamini ndi a Abinere, namwalira mazana atatu mphambu makumi asanu ndi limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Koma ankhondo a Davidewo anali atapha anthu 360 a Abinere, a fuko la Benjamini. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Koma ankhondo a Davide anapha ankhondo a fuko la Benjamini 360 amene anali ndi Abineri. Onani mutuwo |