Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




2 Samueli 2:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo tsikulo nkhondo inakula ndithu. Ndi Abinere ndi anthu a Israele anathawa pamaso pa anyamata a Davide.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo tsikulo nkhondo inakula ndithu. Ndi Abinere ndi anthu a Israele anathawa pamaso pa anyamata a Davide.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Tsono panali nkhondo yoopsa tsiku limenelo. Abinere pamodzi ndi anthu a ku Israele adagonjetsedwa ndi ankhondo a Davide.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Tsiku limeneli nkhondo yake inali yoopsa kwambiri, ndipo Abineri ndi ankhondo a Israeli anagonjetsedwa ndi ankhondo a Davide.

Onani mutuwo Koperani




2 Samueli 2:17
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Abinere ananena ndi Yowabu, Aimirire anyamata nasewere pamaso pathu. Nati Yowabu, Aimirire.


Ndipo anagwirana munthu yense kugwira mutu wa mnzake, nagwaza ndi lupanga lake m'nthiti mwa mnzake. Chomwecho anagwa limodzi; chifukwa chake malo aja anatchedwa Dera la Mipeni la ku Gibiyoni.


Ndipo panali nkhondo nthawi yaitali pakati pa nyumba ya Saulo ndi nyumba ya Davide. Koma Davide analimba chilimbire, ndi nyumba ya Saulo inafooka chifokere.


Chiyambi cha ndeu chifanana ndi kutsegulira madzi; tsono kupikisana kusanayambe tasiya makani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa